Yesaya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu avala ziguduli+ m’misewu yake. Pamadenga*+ ake ndi m’mabwalo a mizinda yake, aliyense akufuula. Akulira n’kumapita kumunsi.+ Yesaya 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Uwu ndi uthenga wokhudza chigwa cha masomphenya:+ Kodi chachitika n’chiyani kuti anthu ako onse akwere pamadenga?+
3 Anthu avala ziguduli+ m’misewu yake. Pamadenga*+ ake ndi m’mabwalo a mizinda yake, aliyense akufuula. Akulira n’kumapita kumunsi.+
22 Uwu ndi uthenga wokhudza chigwa cha masomphenya:+ Kodi chachitika n’chiyani kuti anthu ako onse akwere pamadenga?+