Yesaya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu avala ziguduli+ m’misewu yake. Pamadenga*+ ake ndi m’mabwalo a mizinda yake, aliyense akufuula. Akulira n’kumapita kumunsi.+ Yeremiya 48:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “‘Anthu akulira pamadenga onse a nyumba za ku Mowabu ndi m’mabwalo ake onse.+ Akulira chifukwa ndaphwanya Mowabu ngati chiwiya chimene sichikundikondweretsa,’+ watero Yehova.
3 Anthu avala ziguduli+ m’misewu yake. Pamadenga*+ ake ndi m’mabwalo a mizinda yake, aliyense akufuula. Akulira n’kumapita kumunsi.+
38 “‘Anthu akulira pamadenga onse a nyumba za ku Mowabu ndi m’mabwalo ake onse.+ Akulira chifukwa ndaphwanya Mowabu ngati chiwiya chimene sichikundikondweretsa,’+ watero Yehova.