Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Masomphenya+ amene Yesaya+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu m’masiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+

  • Yesaya 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Uwu ndi uthenga wokhudza Babulo,+ umene Yesaya mwana wa Amozi+ anaona m’masomphenya:

  • Yesaya 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa, wabweretsa tsiku lachisokonezo,+ la kugonjetsedwa+ ndiponso lothetsa nzeru+ m’chigwa cha masomphenya. Kumeneko mpanda ukugwetsedwa+ ndipo kufuula kukumvekera m’phiri.+

  • Yeremiya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti Yehova wa makamu wanena kuti: “Dulani mitengo+ kuti tipangire Yerusalemu chiunda chomenyerapo nkhondo.*+ Yerusalemu ndi mzinda woyenera kuimbidwa mlandu.+ Mkati mwake muli kuponderezana kokhakokha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena