2 Mafumu 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Manase anakhetsanso magazi osalakwa ochuluka zedi,+ mpaka magaziwo anadzaza nawo Yerusalemu kuyambira koyambirira mpaka kumapeto, kuwonjezera pa tchimo lake limene anachimwitsa nalo Yuda mwa kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Ezekieli 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Panga unyolo+ chifukwa dzikolo ladzaza ziweruzo za magazi,+ ndipo mumzindamo mwadzaza chiwawa.+
16 Manase anakhetsanso magazi osalakwa ochuluka zedi,+ mpaka magaziwo anadzaza nawo Yerusalemu kuyambira koyambirira mpaka kumapeto, kuwonjezera pa tchimo lake limene anachimwitsa nalo Yuda mwa kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+