Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 27:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Yehova wandiuza kuti, ‘Upange zomangira ndiponso magoli,+ ndipo uzivale m’khosi mwako.+

  • Yeremiya 39:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mfumu ya Babulo inachititsa khungu maso a Zedekiya+ ndipo kenako inamumanga m’maunyolo amkuwa kuti apite naye ku Babulo.

  • Yeremiya 40:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya, pamene Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anamumasula ku Rama.+ Yeremiya anali womangidwa maunyolo a m’manja pamene Nebuzaradani anamutenga pakati pa anthu a ku Yerusalemu ndi a ku Yuda amene anali kupita ku ukapolo ku Babulo.+

  • Maliro 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Wanditsekereza ngati mmene mpanda wamiyala umatsekerezera, kuti ndisatuluke.+ Wandimanga ndi maunyolo olemera amkuwa.+

  • Nahumu 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma nayenso No-amoni anayenera kutengedwa kupita kudziko lina,+ ndipo anagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo. Ana ake anaphwanyidwaphwanyidwa m’misewu yake yonse+ ndipo anthu ake olemekezeka anawachitira maere.+ Anthu ake onse otchuka anamangidwa m’matangadza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena