Yesaya 59:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukonde wawo wa kangaude sudzakhala chovala chawo, ndipo iwo sadzavala zochita zawo.+ Ntchito zawo n’zopweteka ena, ndipo m’manja mwawo muli ntchito zachiwawa.+ Mika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+
6 Ukonde wawo wa kangaude sudzakhala chovala chawo, ndipo iwo sadzavala zochita zawo.+ Ntchito zawo n’zopweteka ena, ndipo m’manja mwawo muli ntchito zachiwawa.+
2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+