Oweruza 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho Yowasi anatcha Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala*+ pa tsiku limenelo, ndipo anati: “Baala adziweruzire yekha mlandu, chifukwa winawake wagwetsa guwa lake lansembe.”+ Oweruza 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Yerubaala,+ kapena kuti Gidiyoni,+ pamodzi ndi anthu onse amene anali naye, anadzuka m’mawa kwambiri ndi kumanga msasa pachitsime cha Harodi. Msasa wa Amidiyani unali chakumpoto, m’chigwa, kuphiri la More.
32 Choncho Yowasi anatcha Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala*+ pa tsiku limenelo, ndipo anati: “Baala adziweruzire yekha mlandu, chifukwa winawake wagwetsa guwa lake lansembe.”+
7 Pamenepo Yerubaala,+ kapena kuti Gidiyoni,+ pamodzi ndi anthu onse amene anali naye, anadzuka m’mawa kwambiri ndi kumanga msasa pachitsime cha Harodi. Msasa wa Amidiyani unali chakumpoto, m’chigwa, kuphiri la More.