Mlaliki 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso chikondi chawo, chidani chawo ndiponso nsanje yawo zatha kale,+ ndipo alibenso gawo mpaka kalekale pa chilichonse chimene chikuchitika padziko lapansi pano.+ Yesaya 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo afa. Sadzakhalanso ndi moyo.+ Iwo ndi akufa+ ndipo sadzaukanso.+ Pa chifukwa chimenechi, mwawatembenukira kuti muwawononge n’cholinga choti asadzatchulidwenso.+
6 Komanso chikondi chawo, chidani chawo ndiponso nsanje yawo zatha kale,+ ndipo alibenso gawo mpaka kalekale pa chilichonse chimene chikuchitika padziko lapansi pano.+
14 Iwo afa. Sadzakhalanso ndi moyo.+ Iwo ndi akufa+ ndipo sadzaukanso.+ Pa chifukwa chimenechi, mwawatembenukira kuti muwawononge n’cholinga choti asadzatchulidwenso.+