Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munthu akafa, kodi angakhalenso ndi moyo?+

      Ndidzadikira masiku onse a ntchito yanga yokakamiza,+

      Mpaka mpumulo wanga utafika.+

  • Mlaliki 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Komanso chikondi chawo, chidani chawo ndiponso nsanje yawo zatha kale,+ ndipo alibenso gawo mpaka kalekale pa chilichonse chimene chikuchitika padziko lapansi pano.+

  • Yeremiya 51:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 “Chilakolako chawo chikadzakhala champhavu kwambiri ndidzawakonzera mapwando ndipo ndidzawaledzeretsa kuti asangalale.+ Pamenepo adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale, ndipo sadzadzukanso,”+ watero Yehova.

  • Mateyu 25:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena