29 “Amuna inu, abale anga, ndilankhula ndithu mwaufulu za kholo lathu Davide. Iye anamwalira+ ndi kuikidwa m’manda, ndipo manda ake tili nawo mpaka lero.
36 Koma Davide+ anakwaniritsa chifuniro cha Mulungu mu nthawi ya m’badwo wake, ndipo anagona mu imfa ndi kuikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake, moti thupi lake linavunda.+