1 Samueli 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ifenso tikufuna kukhala ngati mitundu ina yonse,+ ndipo mfumu yathuyo ndi imene izitiweruza ndi kutitsogolera kukamenya nkhondo zathu.” 2 Samueli 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli+ yense ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo+ kwa anthu ake onse.+
20 Ifenso tikufuna kukhala ngati mitundu ina yonse,+ ndipo mfumu yathuyo ndi imene izitiweruza ndi kutitsogolera kukamenya nkhondo zathu.”
15 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli+ yense ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo+ kwa anthu ake onse.+