2 Samueli 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno masiku amenewo munthu akalandira malangizo kwa Ahitofeli, zinali ngati kuti munthu wafunsira malangizo kwa Mulungu woona. Umu ndi mmene malangizo+ onse a Ahitofeli+ analili, kwa Davide ndi Abisalomu yemwe. 2 Samueli 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Abisalomu ndi amuna onse a Isiraeli anati: “Malangizo a Husai Mwareki ndi abwino+ kusiyana ndi malangizo a Ahitofeli!” Ndipo Yehova anaonetsetsa+ kuti anthuwo asatsatire malangizo+ a Ahitofeli ngakhale kuti anali abwino.+ Yehova anachita zimenezi kuti adzetsere Abisalomu tsoka.+
23 Ndiyeno masiku amenewo munthu akalandira malangizo kwa Ahitofeli, zinali ngati kuti munthu wafunsira malangizo kwa Mulungu woona. Umu ndi mmene malangizo+ onse a Ahitofeli+ analili, kwa Davide ndi Abisalomu yemwe.
14 Kenako Abisalomu ndi amuna onse a Isiraeli anati: “Malangizo a Husai Mwareki ndi abwino+ kusiyana ndi malangizo a Ahitofeli!” Ndipo Yehova anaonetsetsa+ kuti anthuwo asatsatire malangizo+ a Ahitofeli ngakhale kuti anali abwino.+ Yehova anachita zimenezi kuti adzetsere Abisalomu tsoka.+