1 Samueli 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 (Kalekale mu Isiraeli, munthu akafuna kukafunsira kwa Mulungu ankanena kuti: “Tiyeni tipite kwa wamasomphenya.”*+ Pakuti amene amatchedwa mneneri masiku ano, kalekalelo anali kutchedwa kuti wamasomphenya.) 2 Mbiri 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imeneyo, wamasomphenya* Haneni+ anapita kwa Asa mfumu ya Yuda n’kumuuza kuti: “Chifukwa chakuti munadalira mfumu ya Siriya,+ osadalira Yehova Mulungu wanu,+ gulu lankhondo la mfumu ya Siriya lathawa m’manja mwanu.
9 (Kalekale mu Isiraeli, munthu akafuna kukafunsira kwa Mulungu ankanena kuti: “Tiyeni tipite kwa wamasomphenya.”*+ Pakuti amene amatchedwa mneneri masiku ano, kalekalelo anali kutchedwa kuti wamasomphenya.)
7 Pa nthawi imeneyo, wamasomphenya* Haneni+ anapita kwa Asa mfumu ya Yuda n’kumuuza kuti: “Chifukwa chakuti munadalira mfumu ya Siriya,+ osadalira Yehova Mulungu wanu,+ gulu lankhondo la mfumu ya Siriya lathawa m’manja mwanu.