2 Samueli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika. 2 Samueli 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yowabu anali mtsogoleri wa gulu lonse lankhondo+ la Isiraeli. Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali kutsogolera Akereti+ ndi Apeleti.+ 1 Mafumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anayamba kuchitira zinthu limodzi ndi Yowabu mwana wa Zeruya komanso wansembe Abiyatara.+ Iwowa anayamba kumuthandiza Adoniya+ monga otsatira ake.
16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
23 Yowabu anali mtsogoleri wa gulu lonse lankhondo+ la Isiraeli. Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali kutsogolera Akereti+ ndi Apeleti.+
7 Iye anayamba kuchitira zinthu limodzi ndi Yowabu mwana wa Zeruya komanso wansembe Abiyatara.+ Iwowa anayamba kumuthandiza Adoniya+ monga otsatira ake.