Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Uziopa Yehova Mulungu wako+ ndi kum’tumikira,+ ndipo uzilumbira pa dzina lake.+

  • 1 Samueli 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Motero anthuwo anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa makamu, amene akukhala pa akerubi.+ Ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anali pamenepo ndi likasa la pangano la Mulungu woona.+

  • Salimo 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndani?”

      “Ndi Yehova wa makamu. Iye ndiye Mfumu yaulemerero.”+ [Seʹlah.]

  • Yesaya 49:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Takweza maso ako uone zonse zimene zikuchitika mokuzungulira. Onse asonkhanitsidwa pamodzi.+ Abwera kwa iwe. Yehova wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo,+ onsewo udzadzikongoletsa nawo ngati zokongoletsera, ndipo udzawavala ngati ndiwe mkwatibwi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena