1 Mafumu 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho pamene Yezebeli+ anapha aneneri a Yehova,+ Obadiya anatenga aneneri 100 n’kuwagawa m’magulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga ndipo anali kuwapatsa mkate ndi madzi.)+
4 Choncho pamene Yezebeli+ anapha aneneri a Yehova,+ Obadiya anatenga aneneri 100 n’kuwagawa m’magulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga ndipo anali kuwapatsa mkate ndi madzi.)+