1 Mafumu 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Ndilipo ndekha mneneri wa Yehova amene watsala,+ ndekhandekha basi, koma aneneri a Baala alipo 450. Miyambo 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ukafooka pa tsiku la masautso,+ mphamvu zako zidzakhala zochepa. Aroma 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova, iwo apha aneneri anu, agumula maguwa anu ansembe, moti ine ndatsala ndekhandekha. Tsopano akufunafuna moyo wanga.”+
22 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Ndilipo ndekha mneneri wa Yehova amene watsala,+ ndekhandekha basi, koma aneneri a Baala alipo 450.
3 “Yehova, iwo apha aneneri anu, agumula maguwa anu ansembe, moti ine ndatsala ndekhandekha. Tsopano akufunafuna moyo wanga.”+