Miyambo 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 N’kosayenera kwa mafumu iwe Lemueli, n’kosayenera kuti mafumu azimwa vinyo,+ kapena kuti akuluakulu olemekezeka azinena kuti: “Kodi chakumwa choledzeretsa chili kuti?” Mlaliki 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dziko iwe, ndiwe wodala ngati mfumu yako ili mwana wochokera ku banja lachifumu, ndipo akalonga ako amadya pa nthawi yake kuti akhale amphamvu, osati kumangomwa mopitirira muyezo.+ Hoseya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dama, vinyo wakale ndi vinyo wotsekemera zimawononga nzeru za munthu.+
4 N’kosayenera kwa mafumu iwe Lemueli, n’kosayenera kuti mafumu azimwa vinyo,+ kapena kuti akuluakulu olemekezeka azinena kuti: “Kodi chakumwa choledzeretsa chili kuti?”
17 Dziko iwe, ndiwe wodala ngati mfumu yako ili mwana wochokera ku banja lachifumu, ndipo akalonga ako amadya pa nthawi yake kuti akhale amphamvu, osati kumangomwa mopitirira muyezo.+