1 Mbiri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana wa Solomo anali Rehobowamu.+ Rehobowamu anabereka Abiya,+ Abiya anabereka Asa,+ Asa anabereka Yehosafati,+ 2 Mbiri 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Yehosafati+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake, ndipo analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli. 2 Mbiri 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehosafati+ anapitiriza kulamulira ku Yuda. Iye anali ndi zaka 35 pamene anayamba kulamulira ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 25. Mayi ake dzina lawo linali Azuba+ mwana wa Sili. Mateyu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Asa anabereka Yehosafati.+Yehosafati anabereka Yehoramu.+Yehoramu anabereka Uziya.
10 Mwana wa Solomo anali Rehobowamu.+ Rehobowamu anabereka Abiya,+ Abiya anabereka Asa,+ Asa anabereka Yehosafati,+
17 Ndiyeno Yehosafati+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake, ndipo analimbitsa ufumu wake mu Isiraeli.
31 Yehosafati+ anapitiriza kulamulira ku Yuda. Iye anali ndi zaka 35 pamene anayamba kulamulira ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 25. Mayi ake dzina lawo linali Azuba+ mwana wa Sili.