1 Mafumu 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pomalizira pake, Asa anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake.+ Ndiyeno Yehosafati+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. 1 Mafumu 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yehosafati+ mwana wa Asa anakhala mfumu ya Yuda m’chaka chachinayi cha Ahabu mfumu ya Isiraeli.
24 Pomalizira pake, Asa anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake.+ Ndiyeno Yehosafati+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.