Salimo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwaichititsa kukhala yodalitsika kwambiri mpaka muyaya.+Mwaikondweretsa ndi kuisangalatsa pamaso panu.+ Salimo 72:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+
6 Mwaichititsa kukhala yodalitsika kwambiri mpaka muyaya.+Mwaikondweretsa ndi kuisangalatsa pamaso panu.+
17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+