Salimo 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mudzandidziwitsa njira ya moyo.+Chifukwa cha nkhope yanu, munthu adzakondwera mokwanira.+Kudzanja lanu lamanja kuli chimwemwe mpaka muyaya.+ Salimo 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+ Machitidwe 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwandidziwitsa njira za moyo, ndipo chifukwa cha nkhope yanu ndidzakhala ndi chimwemwe chosefukira.’+
11 Mudzandidziwitsa njira ya moyo.+Chifukwa cha nkhope yanu, munthu adzakondwera mokwanira.+Kudzanja lanu lamanja kuli chimwemwe mpaka muyaya.+
7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+
28 Mwandidziwitsa njira za moyo, ndipo chifukwa cha nkhope yanu ndidzakhala ndi chimwemwe chosefukira.’+