Salimo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwaichititsa kukhala yodalitsika kwambiri mpaka muyaya.+Mwaikondweretsa ndi kuisangalatsa pamaso panu.+ Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Odala ndi anthu oyera mtima,+ chifukwa adzaona Mulungu.+ Machitidwe 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwandidziwitsa njira za moyo, ndipo chifukwa cha nkhope yanu ndidzakhala ndi chimwemwe chosefukira.’+ 1 Timoteyo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chiphunzitso chimenechi n’chogwirizana ndi uthenga wabwino waulemerero umene anauika m’manja mwanga,+ wochokera kwa Mulungu wachimwemwe.+
6 Mwaichititsa kukhala yodalitsika kwambiri mpaka muyaya.+Mwaikondweretsa ndi kuisangalatsa pamaso panu.+
28 Mwandidziwitsa njira za moyo, ndipo chifukwa cha nkhope yanu ndidzakhala ndi chimwemwe chosefukira.’+
11 Chiphunzitso chimenechi n’chogwirizana ndi uthenga wabwino waulemerero umene anauika m’manja mwanga,+ wochokera kwa Mulungu wachimwemwe.+