Salimo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Miyambo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 M’njira yachilungamo muli moyo,+ ndipo ulendo wa m’njira imeneyi suthera ku imfa.+
4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+