Miyambo 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 pakuti chuma sichidzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo chisoti chachifumu sichidzakhalapo ku mibadwo yonse. 1 Timoteyo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe, anthu ofunitsitsa kulemera, amagwera m’mayesero+ ndi mumsampha. Iwo amakodwa ndi zilakolako zambiri zowapweteketsa ndiponso amachita zinthu mopanda nzeru.+ Zinthu zimenezi zimawawononga ndi kuwabweretsera mavuto.+
24 pakuti chuma sichidzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo chisoti chachifumu sichidzakhalapo ku mibadwo yonse.
9 Komabe, anthu ofunitsitsa kulemera, amagwera m’mayesero+ ndi mumsampha. Iwo amakodwa ndi zilakolako zambiri zowapweteketsa ndiponso amachita zinthu mopanda nzeru.+ Zinthu zimenezi zimawawononga ndi kuwabweretsera mavuto.+