Miyambo 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi maso ako amayang’anitsitsa chuma, pomwe icho sichichedwa kuchoka?+ Chifukwa ndithu chimadzipangira mapiko ngati a chiwombankhanga n’kuulukira kumwamba.+ 1 Timoteyo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+ Yakobo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo wachuma+ akondwere chifukwa tsopano watsitsidwa, chifukwa mofanana ndi duwa la zomera, wachumayo adzafota.+
5 Kodi maso ako amayang’anitsitsa chuma, pomwe icho sichichedwa kuchoka?+ Chifukwa ndithu chimadzipangira mapiko ngati a chiwombankhanga n’kuulukira kumwamba.+
17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+
10 ndipo wachuma+ akondwere chifukwa tsopano watsitsidwa, chifukwa mofanana ndi duwa la zomera, wachumayo adzafota.+