Genesis 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Motero Mulungu anapanga nyama zakutchire monga mwa mitundu yake. Anapanganso nyama zoweta monga mwa mitundu yake, komanso nyama iliyonse yokwawa panthaka monga mwa mtundu wake.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino. Miyambo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pita kwa nyerere+ waulesi iwe,+ ukaone mmene imachitira zinthu kuti ukhale wanzeru. Miyambo 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nyerere si zamphamvu,+ koma zimasonkhanitsa chakudya chawo m’chilimwe.+
25 Motero Mulungu anapanga nyama zakutchire monga mwa mitundu yake. Anapanganso nyama zoweta monga mwa mitundu yake, komanso nyama iliyonse yokwawa panthaka monga mwa mtundu wake.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.