Miyambo 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Monga mmene amakhalira vinyo wowawasa m’mano ndiponso utsi m’maso, ndi mmenenso amakhalira munthu waulesi kwa amene am’tuma.+ Miyambo 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Waulesi amati: “Panjira pali mkango wamphamvu. M’mabwalo a mzinda mukuyendayenda mkango.”+
26 Monga mmene amakhalira vinyo wowawasa m’mano ndiponso utsi m’maso, ndi mmenenso amakhalira munthu waulesi kwa amene am’tuma.+