Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 41:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zipinda za mzere wachiwiri zinali zokulirapo m’mbali kuposa za mzere woyamba, ndipo zipinda za mzere wachitatu zinali zokulirapo m’mbali kuposa za mzere wachiwiri. Panali masitepe oyenda chozungulira opitira m’zipinda zam’mwamba.+ Choncho zipinda za mzere wachitatu zinali zokulirapo kuposa zipinda za mzere wachiwiri, ndipo zipinda za mzere wachiwiri zinali zokulirapo kuposa za mzere woyamba. Munthu akafuna kupita kuzipinda zam’mwamba kuchokera kuzipinda zapansi+ anali kudutsa m’zipinda zapakati.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena