Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 31:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo ndidzam’patsa mzimu wa Mulungu kuti akhale wanzeru, wozindikira, wodziwa zinthu, ndi kuti akhale mmisiri waluso pa ntchito ina iliyonse.+

  • Ekisodo 35:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndipo anam’patsa mzimu wa Mulungu kuti akhale wanzeru, wozindikira, wodziwa zinthu, ndi kuti akhale mmisiri waluso pa ntchito ina iliyonse.

  • Ekisodo 36:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 “Bezaleli komanso Oholiabu+ ndi mwamuna aliyense wa mtima wanzeru amene Yehova wam’patsa nzeru+ ndi kuzindikira+ pa zinthu zimenezi, ayenera kugwira ntchitoyi. Iwowa apatsidwa nzeru ndi kuzindikira kuti adziwe kuchita ntchito zonse zopatulika motsatira zonse zimene Yehova walamula.”+

  • Danieli 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano Mulungu anawachititsa ana anayi amenewa kudziwa ndi kuzindikira zinthu zonse zolembedwa ndiponso anawapatsa nzeru.+ Danieli anali womvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena