Deuteronomo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo iwe ukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wako ndi Mulungu woona,+ Mulungu wokhulupirika,+ wosunga pangano+ ndiponso wosonyeza kukoma mtima kosatha kwa anthu amene amam’konda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo masauzande,+ Nehemiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, ndinu Mulungu wamkulu ndi wochititsa mantha.+ Anthu amene amakukondani+ ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha.
9 Ndipo iwe ukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wako ndi Mulungu woona,+ Mulungu wokhulupirika,+ wosunga pangano+ ndiponso wosonyeza kukoma mtima kosatha kwa anthu amene amam’konda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo masauzande,+
5 Pamenepo ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, ndinu Mulungu wamkulu ndi wochititsa mantha.+ Anthu amene amakukondani+ ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha.