Numeri 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Aamaleki+ amakhala ku Negebu.+ Ahiti, Ayebusi+ ndi Aamori+ amakhala kudera lamapiri. Akanani+ amakhala m’mphepete mwa nyanja, ndi m’mphepete mwa mtsinje wa Yorodano.” Oweruza 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Benjamini sanapitikitse Ayebusi amene anali kukhala m’Yerusalemu,+ moti Ayebusiwo akukhalabe ndi ana a Benjamini m’Yerusalemu kufikira lero.+
29 Aamaleki+ amakhala ku Negebu.+ Ahiti, Ayebusi+ ndi Aamori+ amakhala kudera lamapiri. Akanani+ amakhala m’mphepete mwa nyanja, ndi m’mphepete mwa mtsinje wa Yorodano.”
21 Ana a Benjamini sanapitikitse Ayebusi amene anali kukhala m’Yerusalemu,+ moti Ayebusiwo akukhalabe ndi ana a Benjamini m’Yerusalemu kufikira lero.+