Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 2:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Koma Mfumu Solomo idzadalitsidwa,+ ndipo mpando wachifumu wa Davide udzakhazikika kwamuyaya pamaso pa Yehova.”+

  • 2 Mbiri 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Adalitsike Yehova Mulungu wanu,+ amene wasangalala+ nanu mwa kukuikani pampando wake wachifumu+ monga mfumu yolamulira m’malo mwa Yehova Mulungu wanu.+ Popeza Mulungu wanu anakonda+ Isiraeli kuti akhalepo mpaka kalekale, wakuikani kuti mukhale mfumu yawo,+ kuti muzipereka zigamulo+ ndi kuchita chilungamo.”+

  • Luka 11:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Mfumukazi+ ya kum’mwera adzaiimiritsa pa chiweruzo limodzi ndi anthu a m’badwo uwu, ndipo idzawatsutsa. Chifukwa mfumukazi imeneyi inabwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi kudzamva nzeru za Solomo. Koma tsopano wina woposa+ Solomo ali pano.

  • Yohane 1:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Natanayeli anamuyankha kuti: “Rabi, ndinudi Mwana wa Mulungu,+ ndinu Mfumu+ ya Isiraeli.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena