Ezara 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Bisilamu, Mitiredati, Tabeeli, ndi anzake ena onse analemba kalata kwa Aritasasita mfumu ya Perisiya m’masiku a mfumuyo. Kalatayo anaimasulira m’Chiaramu n’kuilemba m’zilembo za Chiaramu.+ Danieli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Akasidi anayankha mfumu m’chinenero cha Chiaramu+ kuti: “Inu mfumu mukhale ndi moyo mpaka kalekale.*+ Tiuzeni ife atumiki anu zimene mwalota ndipo tikumasulirani malotowo.”+
7 Bisilamu, Mitiredati, Tabeeli, ndi anzake ena onse analemba kalata kwa Aritasasita mfumu ya Perisiya m’masiku a mfumuyo. Kalatayo anaimasulira m’Chiaramu n’kuilemba m’zilembo za Chiaramu.+
4 Pamenepo Akasidi anayankha mfumu m’chinenero cha Chiaramu+ kuti: “Inu mfumu mukhale ndi moyo mpaka kalekale.*+ Tiuzeni ife atumiki anu zimene mwalota ndipo tikumasulirani malotowo.”+