2 Mbiri 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera. Ezara 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ndiye tinganene chiyani inu Mulungu wathu pambuyo pa zimene zachitikazi? Popeza tasiya malamulo anu+
16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera.
10 “Ndiye tinganene chiyani inu Mulungu wathu pambuyo pa zimene zachitikazi? Popeza tasiya malamulo anu+