1 Mafumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Davide anagona limodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide.+ 2 Mafumu 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pomalizira pake, Hezekiya anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Manase+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
21 Pomalizira pake, Hezekiya anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Manase+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.