Ekisodo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Koma ngati munthu wabwereka chiweto kwa mnzake+ ndipo chalumala kapena chafa mwiniwake palibe, wobwerekayo azilipira ndithu.+ 2 Mafumu 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anapita kwa munthu wa Mulungu woona uja kukamuuza zomwe zinachitikazo. Munthu wa Mulungu woonayo anati: “Pita ukagulitse mafutawo ndi kubweza ngongole zako,+ ndipo ndalama zotsalazo zithandize iwe ndi ana ako.”+
14 “Koma ngati munthu wabwereka chiweto kwa mnzake+ ndipo chalumala kapena chafa mwiniwake palibe, wobwerekayo azilipira ndithu.+
7 Kenako anapita kwa munthu wa Mulungu woona uja kukamuuza zomwe zinachitikazo. Munthu wa Mulungu woonayo anati: “Pita ukagulitse mafutawo ndi kubweza ngongole zako,+ ndipo ndalama zotsalazo zithandize iwe ndi ana ako.”+