2 Mafumu 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pomalizira pake, Yehoramu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Kenako mwana wake Ahaziya+ anayamba kulamulira m’malo mwake. 2 Mbiri 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anayamba kulamulira+ ali ndi zaka 22 ndipo analamulira ku Yerusalemu chaka chimodzi. Amayi ake dzina lawo linali Ataliya+ mdzukulu wa Omuri.+
24 Pomalizira pake, Yehoramu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Kenako mwana wake Ahaziya+ anayamba kulamulira m’malo mwake.
2 Iye anayamba kulamulira+ ali ndi zaka 22 ndipo analamulira ku Yerusalemu chaka chimodzi. Amayi ake dzina lawo linali Ataliya+ mdzukulu wa Omuri.+