2 Mafumu 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Elisa+ anadwala matenda amene pamapeto pake anafa nawo.+ Choncho Yehoasi mfumu ya Isiraeli anapita kwa iye n’kuyamba kulira atam’kumbatira n’kumati: “Bambo anga,+ bambo anga! Galeta lankhondo la Isiraeli ndi okwera pamahatchi ake!”+
14 Tsopano Elisa+ anadwala matenda amene pamapeto pake anafa nawo.+ Choncho Yehoasi mfumu ya Isiraeli anapita kwa iye n’kuyamba kulira atam’kumbatira n’kumati: “Bambo anga,+ bambo anga! Galeta lankhondo la Isiraeli ndi okwera pamahatchi ake!”+