1 Mafumu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ukadzozenso Yehu+ mdzukulu wa Nimusi+ kuti akhale mfumu ya Isiraeli, ndipo Elisa+ mwana wa Safati wa ku Abele-mehola,+ ukam’dzoze kuti akhale mneneri m’malo mwa iwe.+ 2 Mafumu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Elisa munthu wa Mulungu woona atangomva kuti mfumu ya Isiraeli yang’amba zovala zake,+ anatumiza uthenga kwa mfumuyo, wakuti: “N’chifukwa chiyani mwang’amba zovala zanu? Muuzeni abwere kwa ine kuti adziwe kuti ku Isiraeli kuli mneneri.”+
16 Ukadzozenso Yehu+ mdzukulu wa Nimusi+ kuti akhale mfumu ya Isiraeli, ndipo Elisa+ mwana wa Safati wa ku Abele-mehola,+ ukam’dzoze kuti akhale mneneri m’malo mwa iwe.+
8 Elisa munthu wa Mulungu woona atangomva kuti mfumu ya Isiraeli yang’amba zovala zake,+ anatumiza uthenga kwa mfumuyo, wakuti: “N’chifukwa chiyani mwang’amba zovala zanu? Muuzeni abwere kwa ine kuti adziwe kuti ku Isiraeli kuli mneneri.”+