2 Mbiri 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano mfumuyo inawauza zochita ndipo anapanga bokosi+ n’kuliika panja, pachipata cha nyumba ya Yehova. Maliko 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno anakhala pansi moyang’anana ndi moponyamo zopereka+ ndipo anali kuona mmene khamu la anthu linali kuponyera ndalama moponya zoperekamo. Anthu ambiri olemera anali kuponyamo makobidi ambiri.+ Luka 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano atakweza maso anaona anthu olemera akuponya zopereka zawo moponyamo zopereka.+
8 Tsopano mfumuyo inawauza zochita ndipo anapanga bokosi+ n’kuliika panja, pachipata cha nyumba ya Yehova.
41 Ndiyeno anakhala pansi moyang’anana ndi moponyamo zopereka+ ndipo anali kuona mmene khamu la anthu linali kuponyera ndalama moponya zoperekamo. Anthu ambiri olemera anali kuponyamo makobidi ambiri.+