2 Mbiri 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akalonga onse+ ndi anthu onse anayamba kusangalala,+ ndipo anali kubweretsa ndalama za msonkhowo n’kumaziponya m’bokosi+ lija kufikira aliyense anapereka. Mateyu 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 kuti mphatso zako zachifundo zikhale zamseri. Ukatero Atate wako amene akuyang’ana kuseriko adzakubwezera.+ 2 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+
10 Akalonga onse+ ndi anthu onse anayamba kusangalala,+ ndipo anali kubweretsa ndalama za msonkhowo n’kumaziponya m’bokosi+ lija kufikira aliyense anapereka.
4 kuti mphatso zako zachifundo zikhale zamseri. Ukatero Atate wako amene akuyang’ana kuseriko adzakubwezera.+
7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+