Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 18:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Davide pamodzi ndi asilikali ake ananyamuka, ndipo anakapha+ amuna 200 achifilisiti. Ndiyeno Davide anabwerako atatenga makungu awo a kunsonga,+ ndipo makungu onsewo anawapereka kwa mfumu kuti achite naye mgwirizano wa ukwati. Pamenepo Sauli anapereka Mikala, mwana wake wamkazi, kwa Davide kuti akhale mkazi wake.+

  • 2 Samueli 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Davide anamuyankha kuti: “Chabwino! Ineyo ndichitadi nawe pangano. Koma ndikukupempha chinthu chimodzi ichi, ‘Usadzaone nkhope yanga+ pokhapokha utabweretsa Mikala,+ mwana wamkazi wa Sauli pobwera kuno.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena