Genesis 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Yuda anauza bambo ake kuti:+ “Munthu ujatu anatichenjeza mwamphamvu kuti, ‘Musadzayese n’komwe kuonekeranso pamaso panga mukadzalephera kubwera naye m’bale wanuyo.’+ Genesis 44:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma ife tinati, ‘Sitingathe kutsikira kumeneko. Ngati tikhala naye limodzi mng’ono wathuyu tipitako, chifukwa sitingathe kukaonekeranso pamaso pa munthuyo tikapanda kupita naye.’+
3 Koma Yuda anauza bambo ake kuti:+ “Munthu ujatu anatichenjeza mwamphamvu kuti, ‘Musadzayese n’komwe kuonekeranso pamaso panga mukadzalephera kubwera naye m’bale wanuyo.’+
26 Koma ife tinati, ‘Sitingathe kutsikira kumeneko. Ngati tikhala naye limodzi mng’ono wathuyu tipitako, chifukwa sitingathe kukaonekeranso pamaso pa munthuyo tikapanda kupita naye.’+