1 Samueli 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Akisi anawafunsa kuti: “Kodi amunanu, lero munakamenya kuti nkhondo?” Poyankha, Davide anati:+ “Kum’mwera kwa dziko la Yuda,+ kum’mwera kwa dziko la Yerameeli+ ndi kum’mwera kwa Akeni.”+
10 Ndiyeno Akisi anawafunsa kuti: “Kodi amunanu, lero munakamenya kuti nkhondo?” Poyankha, Davide anati:+ “Kum’mwera kwa dziko la Yuda,+ kum’mwera kwa dziko la Yerameeli+ ndi kum’mwera kwa Akeni.”+