Deuteronomo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uzipita kwa ansembe+ achilevi ndi kwa woweruza+ amene aziweruza m’masiku amenewo. Uziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuza chigamulo.+ 2 Mbiri 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ku Yerusalemu nakonso Yehosafati anaikako Alevi ena,+ ansembe,+ ndi ena mwa atsogoleri a nyumba za makolo+ a Isiraeli, kuti azionetsetsa kuti anthu akutsatira chilamulo+ cha Yehova ndi kuti aziweruza milandu+ ya anthu a ku Yerusalemu.
9 Uzipita kwa ansembe+ achilevi ndi kwa woweruza+ amene aziweruza m’masiku amenewo. Uziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuza chigamulo.+
8 Ku Yerusalemu nakonso Yehosafati anaikako Alevi ena,+ ansembe,+ ndi ena mwa atsogoleri a nyumba za makolo+ a Isiraeli, kuti azionetsetsa kuti anthu akutsatira chilamulo+ cha Yehova ndi kuti aziweruza milandu+ ya anthu a ku Yerusalemu.