Deuteronomo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 anthu awiri otsutsanawo aziima pamaso pa Yehova, pamaso pa ansembe ndi oweruza amene aziweruza masiku amenewo.+ Deuteronomo 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ansembe, ana a Levi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti am’tumikire+ ndi kudalitsa+ m’dzina la Yehova. Iwo ndiwo ayenera kuthetsa mkangano uliwonse wokhudza choipa chilichonse chimene chachitika.+ Hagai 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Funsa ansembe zokhudza chilamulo.+ Uwafunse kuti: Malaki 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+
17 anthu awiri otsutsanawo aziima pamaso pa Yehova, pamaso pa ansembe ndi oweruza amene aziweruza masiku amenewo.+
5 “Ansembe, ana a Levi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti am’tumikire+ ndi kudalitsa+ m’dzina la Yehova. Iwo ndiwo ayenera kuthetsa mkangano uliwonse wokhudza choipa chilichonse chimene chachitika.+
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+