-
Ekisodo 17:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Manja a Mose atatopa, anatenga mwala ndi kumuikira, ndipo anakhalapo. Aroni ndi Hura anachirikiza manja ake, wina mbali ina winanso mbali ina, moti manja ake anakhalabe choncho mpaka dzuwa kulowa.
-