Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 3:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndinu amene mwayamba kuchititsa atumiki anu kuti aone ukulu wanu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene akuchita ntchito ngati zanu, ndiponso ntchito zamphamvu ngati zanu?+

  • Aefeso 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 ndi kukula kwa mphamvu zake zopambana+ zimene wazipereka kwa ife okhulupirira. Kukula kumeneko n’kogwirizana ndi ntchito+ ya mphamvu yake yodabwitsa,

  • Chivumbulutso 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti:

      “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena