Miyambo 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Milomo yonena zabwino mwachiphamaso koma mumtima muli zoipa, ili ngati siliva wokutira phale.+ Yesaya 41:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ine ndautsa winawake kuchokera kumpoto, ndipo abwera.+ Iye adzaitana pa dzina langa kuchokera kotulukira dzuwa.+ Adzaukira atsogoleri ngati kuti ndi dongo+ ndiponso ngati kuti iyeyo ndi woumba amene amapondaponda dongo laliwisi. Maliro 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana okondedwa a Ziyoni+ amene anali amtengo wapatali ngati golide woyengeka bwino,Tsopano ayamba kuonedwa ngati mitsuko ikuluikulu yadothi, ntchito ya manja a munthu woumba mbiya.+
25 “Ine ndautsa winawake kuchokera kumpoto, ndipo abwera.+ Iye adzaitana pa dzina langa kuchokera kotulukira dzuwa.+ Adzaukira atsogoleri ngati kuti ndi dongo+ ndiponso ngati kuti iyeyo ndi woumba amene amapondaponda dongo laliwisi.
2 Ana okondedwa a Ziyoni+ amene anali amtengo wapatali ngati golide woyengeka bwino,Tsopano ayamba kuonedwa ngati mitsuko ikuluikulu yadothi, ntchito ya manja a munthu woumba mbiya.+